Salimo 44:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Nyamukani. N’chifukwa chiyani mukugonabe, inu Yehova?+Dzukani. Musatitaye kwamuyaya.+ Yesaya 59:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 59 Dzanja la Yehova silinafupike moti n’kulephera kupulumutsa,+ komanso khutu lake silinagonthe moti n’kulephera kumva.+
59 Dzanja la Yehova silinafupike moti n’kulephera kupulumutsa,+ komanso khutu lake silinagonthe moti n’kulephera kumva.+