Salimo 79:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Atsanula magazi awo ngati madziKuzungulira Yerusalemu yense, ndipo palibe wowaika m’manda.+ Yeremiya 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Unene kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Mitembo ya anthu idzangoti mbwee panthaka ngati manyowa. Idzakhala ngati tirigu amene angomumweta kumene koma palibe munthu womusonkhanitsa pamodzi.”’”+
22 “Unene kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Mitembo ya anthu idzangoti mbwee panthaka ngati manyowa. Idzakhala ngati tirigu amene angomumweta kumene koma palibe munthu womusonkhanitsa pamodzi.”’”+