Miyambo 1:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Chotero adzadya zipatso za njira yawo,+ ndipo adzakhuta malangizo awo.+ Yeremiya 4:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Udzalipira chifukwa cha khalidwe lako ndi zochita zako.+ Limeneli ndilo tsoka lako chifukwa zidzakhala zowawa. Zidzatero chifukwa kupanduka kwako kwalowerera mpaka mumtima.”
18 “Udzalipira chifukwa cha khalidwe lako ndi zochita zako.+ Limeneli ndilo tsoka lako chifukwa zidzakhala zowawa. Zidzatero chifukwa kupanduka kwako kwalowerera mpaka mumtima.”