Yeremiya 20:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Nthawi zonse ndikalankhula mawu anu ndimalira. Ndimanena za chiwawa ndi kufunkhidwa,+ pakuti mawu a Yehova achititsa kuti ndizinyozedwa ndi kutonzedwa tsiku lonse.+
8 Nthawi zonse ndikalankhula mawu anu ndimalira. Ndimanena za chiwawa ndi kufunkhidwa,+ pakuti mawu a Yehova achititsa kuti ndizinyozedwa ndi kutonzedwa tsiku lonse.+