Maliro 4:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Akutisakasaka kulikonse kumene tikupita,+ moti palibe amene akuyenda m’mabwalo a mizinda yathu.Mapeto athu ayandikira. Masiku athu akwanira, pakuti mapeto athu afika.+
18 Akutisakasaka kulikonse kumene tikupita,+ moti palibe amene akuyenda m’mabwalo a mizinda yathu.Mapeto athu ayandikira. Masiku athu akwanira, pakuti mapeto athu afika.+