Amosi 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 ‘Pa tsiku limene ndidzalanga Isiraeli+ chifukwa cha kupanduka kwake, ndidzaperekanso chiweruzo pamaguwa ansembe a ku Beteli+ ndipo nyanga za guwa lansembe zidzazulidwa ndi kugwa pansi.+
14 ‘Pa tsiku limene ndidzalanga Isiraeli+ chifukwa cha kupanduka kwake, ndidzaperekanso chiweruzo pamaguwa ansembe a ku Beteli+ ndipo nyanga za guwa lansembe zidzazulidwa ndi kugwa pansi.+