Deuteronomo 10:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Iye ndi amene muyenera kum’tamanda,+ ndipo iye ndi Mulungu wanu amene wakuchitirani zinthu zazikulu ndi zochititsa mantha, zimene mwaziona ndi maso anu.+ Salimo 109:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 109 Inu Mulungu amene ndimakutamandani,+ musakhale chete.+
21 Iye ndi amene muyenera kum’tamanda,+ ndipo iye ndi Mulungu wanu amene wakuchitirani zinthu zazikulu ndi zochititsa mantha, zimene mwaziona ndi maso anu.+