Yesaya 3:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Zipata zake zidzalira+ ndipo zidzamva chisoni. Iye adzatsala wopanda chilichonse. Adzakhala pansi, padothi penipeni.”+ Maliro 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Akuluakulu a mwana wamkazi wa Ziyoni akhala pansi ndipo akhala chete.+Iwo athira fumbi pamitu+ yawo ndipo avala ziguduli.*+Anamwali a Yerusalemu aweramitsa mitu yawo mpaka padothi.+
26 Zipata zake zidzalira+ ndipo zidzamva chisoni. Iye adzatsala wopanda chilichonse. Adzakhala pansi, padothi penipeni.”+
10 Akuluakulu a mwana wamkazi wa Ziyoni akhala pansi ndipo akhala chete.+Iwo athira fumbi pamitu+ yawo ndipo avala ziguduli.*+Anamwali a Yerusalemu aweramitsa mitu yawo mpaka padothi.+