Salimo 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Maso anga achita mdima chifukwa cha chisoni changa.+Maso anga akalamba chifukwa cha anthu onse ondichitira zoipa.+ Maliro 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndikulirira zinthu zimenezi ngati mkazi.+ Maso anga ine! Maso anga akutuluka misozi.+Pakuti wonditonthoza, munthu woti anditsitsimule, ali kutali ndi ine.Ana anga asiyidwa+ popanda thandizo, pakuti mdani wanga wadzitukumula.+ Maliro 3:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Maso anga akungotuluka misozi ngati mtsinje chifukwa cha kuwonongedwa kwa mwana wamkazi wa anthu anga.+
7 Maso anga achita mdima chifukwa cha chisoni changa.+Maso anga akalamba chifukwa cha anthu onse ondichitira zoipa.+
16 Ndikulirira zinthu zimenezi ngati mkazi.+ Maso anga ine! Maso anga akutuluka misozi.+Pakuti wonditonthoza, munthu woti anditsitsimule, ali kutali ndi ine.Ana anga asiyidwa+ popanda thandizo, pakuti mdani wanga wadzitukumula.+
48 Maso anga akungotuluka misozi ngati mtsinje chifukwa cha kuwonongedwa kwa mwana wamkazi wa anthu anga.+