Yeremiya 11:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Yehova wa makamu wanena kuti: “Tsopano ndikuwapatsa chilango. Anyamata adzafa ndi lupanga.+ Ana awo aamuna ndi aakazi adzafa ndi njala yaikulu.+ Maliro 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Nyamuka! Lira mofuula usiku, pa nthawi yoyamba ulonda+ wam’mawa.Khuthula+ mtima wako pamaso+ pa Yehova ngati madzi.Pemphera utakweza manja+ ako kwa iye chifukwa cha ana ako,Amene akukomoka ndi njala m’misewu.+ Maliro 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Lilime la ana oyamwa lamamatira kummero chifukwa cha ludzu.+Ana apempha chakudya+ koma palibe amene akuwapatsa.+
22 Yehova wa makamu wanena kuti: “Tsopano ndikuwapatsa chilango. Anyamata adzafa ndi lupanga.+ Ana awo aamuna ndi aakazi adzafa ndi njala yaikulu.+
19 Nyamuka! Lira mofuula usiku, pa nthawi yoyamba ulonda+ wam’mawa.Khuthula+ mtima wako pamaso+ pa Yehova ngati madzi.Pemphera utakweza manja+ ako kwa iye chifukwa cha ana ako,Amene akukomoka ndi njala m’misewu.+
4 Lilime la ana oyamwa lamamatira kummero chifukwa cha ludzu.+Ana apempha chakudya+ koma palibe amene akuwapatsa.+