Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 28:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Udzafufuzafufuza masana ngati mmene wakhungu amafufuzirafufuzira mu mdima,+ ndipo sudzapambana. Iwe wekha udzakhala wodyeredwa ndi kulandidwa zinthu nthawi zonse, popanda wokupulumutsa.+

  • Yesaya 59:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 N’chifukwa chake chilungamo chatitalikira kwambiri, ndipo zolungama sizikutipeza. Tinali kuyembekezera kuunika koma m’malomwake tikungoona mdima. Tinali kuyembekezera kuwala koma tikungoyendabe mu mdima wosatha.+

  • Yeremiya 13:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Patsani Yehova Mulungu wanu ulemerero+ asanachititse mdima,+ komanso mapazi anu asanapunthwe pamapiri madzulo dzuwa litalowa.+ Mudzayembekeza kuwala+ koma iye adzabweretsa mdima,+ ndipo adzachititsa mdima wandiweyani.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena