Salimo 88:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndakhala womasuka ngati anthu akufa,+Ngati anthu ophedwa amene agona m’manda,+Anthu amene simukuwakumbukiransoKomanso amene sakulandira thandizo kuchokera m’manja mwanu.+ Salimo 143:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mdani akufunafuna moyo wanga,+Iye waupondaponda pafumbi.+Wandichititsa kukhala m’malo a mdima ngati anthu amene anafa kalekale.+
5 Ndakhala womasuka ngati anthu akufa,+Ngati anthu ophedwa amene agona m’manda,+Anthu amene simukuwakumbukiransoKomanso amene sakulandira thandizo kuchokera m’manja mwanu.+
3 Mdani akufunafuna moyo wanga,+Iye waupondaponda pafumbi.+Wandichititsa kukhala m’malo a mdima ngati anthu amene anafa kalekale.+