Yobu 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pakuti mivi ya Wamphamvuyonse yandilasa,+Ndipo ine ndikumwa poizoni wa miviyo.+Zoopsa zochokera kwa Mulungu zasonkhana kuti zilimbane nane.+ Yobu 16:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Anthu ake oponya mivi ndi uta+ andizungulira.Iye wandiboola impso+ koma osamva chisoni,Wakhuthulira ndulu yanga pansi.
4 Pakuti mivi ya Wamphamvuyonse yandilasa,+Ndipo ine ndikumwa poizoni wa miviyo.+Zoopsa zochokera kwa Mulungu zasonkhana kuti zilimbane nane.+
13 Anthu ake oponya mivi ndi uta+ andizungulira.Iye wandiboola impso+ koma osamva chisoni,Wakhuthulira ndulu yanga pansi.