Genesis 41:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Koma pambuyo pa zaka zimenezo, ndithudi padzabwera zaka 7 za njala. Chakudya chonse chochuluka chija m’dziko la Iguputo sichidzakumbukika m’pang’ono pomwe, ndipo njalayo idzawononga dziko lonse.+
30 Koma pambuyo pa zaka zimenezo, ndithudi padzabwera zaka 7 za njala. Chakudya chonse chochuluka chija m’dziko la Iguputo sichidzakumbukika m’pang’ono pomwe, ndipo njalayo idzawononga dziko lonse.+