Salimo 77:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndidzakumbukira zochita za Ya,+Ndithu ndidzakumbukira ntchito yanu yodabwitsa yakale.+