Yesaya 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chotero anthu anga adzapita ku ukapolo kudziko lina chifukwa chosadziwa zinthu.+ Anthu awo olemekezeka adzakhala amuna anjala+ ndipo khamu lawo lidzakhala louma kukhosi ndi ludzu.+
13 Chotero anthu anga adzapita ku ukapolo kudziko lina chifukwa chosadziwa zinthu.+ Anthu awo olemekezeka adzakhala amuna anjala+ ndipo khamu lawo lidzakhala louma kukhosi ndi ludzu.+