Salimo 69:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Pakuti Yehova akumvetsera osauka,+Ndipo sadzanyoza anthu ake amene ali m’ndende.+ Salimo 79:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mverani kuusa moyo kwa mkaidi.+Anthu opita kukaphedwa muwateteze ndi dzanja lanu lamphamvu.+ Salimo 102:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kuti amve kuusa moyo kwa akaidi,+Ndi kumasula anthu opita kukaphedwa.+