Deuteronomo 28:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Pamenepo udzasokonezeka mutu chifukwa cha zimene maso ako adzaona.+ Yeremiya 14:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndipo ndikapita kunja kwa mzinda, ndikuona anthu ophedwa ndi lupanga.+ Komanso ndikalowa mkati mwa mzinda ndikuona matenda obwera chifukwa cha njala.+ Aneneri ndi ansembe, onse ayenda njira zosiyanasiyana kupita kudziko limene sakulidziwa.’”+
18 Ndipo ndikapita kunja kwa mzinda, ndikuona anthu ophedwa ndi lupanga.+ Komanso ndikalowa mkati mwa mzinda ndikuona matenda obwera chifukwa cha njala.+ Aneneri ndi ansembe, onse ayenda njira zosiyanasiyana kupita kudziko limene sakulidziwa.’”+