1 Samueli 26:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tsopano musalole kuti magazi anga akhetsedwe pamaso pa Yehova,+ pakuti mfumu ya Isiraeli yapita kukasakasaka nthata imodzi,+ monga munthu wothamangitsa nkhwali imodzi m’mapiri.”+ Salimo 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ine ndathawira kwa Yehova.+Kodi mulibe mantha? Mukundiuza kuti:“Thawirani kumapiri anu ngati mbalame!+
20 Tsopano musalole kuti magazi anga akhetsedwe pamaso pa Yehova,+ pakuti mfumu ya Isiraeli yapita kukasakasaka nthata imodzi,+ monga munthu wothamangitsa nkhwali imodzi m’mapiri.”+
11 Ine ndathawira kwa Yehova.+Kodi mulibe mantha? Mukundiuza kuti:“Thawirani kumapiri anu ngati mbalame!+