Salimo 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova adzapereka chigamulo ku mitundu ya anthu.+Ndiweruzeni inu Yehova, mogwirizana ndi chilungamo changa,+Komanso mogwirizana ndi mtima wanga wosagawanika.+ Salimo 35:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Weruzani mlandu wanga inu Yehova, motsutsana ndi adani anga.+Menyani nkhondo ndi kugonjetsa amene akumenyana ndi ine.+ Salimo 69:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Yandikirani moyo wanga ndi kuupulumutsa.+Ndiwomboleni kwa adani anga.+ Yeremiya 11:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma Yehova wa makamu amaweruza mwachilungamo.+ Amafufuza impso ndi mtima.+ Inu Mulungu, ndiloleni ndione mukuwapatsa chilango, pakuti ine ndakufotokozerani mlandu wanga.+ Yeremiya 51:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Choncho Yehova wanena kuti: “Ine ndikukuyankhira mlandu,+ ndipo ndidzakubwezerera chilango.+ Ndidzaphwetsa nyanja yake ndi zitsime zake.+
8 Yehova adzapereka chigamulo ku mitundu ya anthu.+Ndiweruzeni inu Yehova, mogwirizana ndi chilungamo changa,+Komanso mogwirizana ndi mtima wanga wosagawanika.+
35 Weruzani mlandu wanga inu Yehova, motsutsana ndi adani anga.+Menyani nkhondo ndi kugonjetsa amene akumenyana ndi ine.+
20 Koma Yehova wa makamu amaweruza mwachilungamo.+ Amafufuza impso ndi mtima.+ Inu Mulungu, ndiloleni ndione mukuwapatsa chilango, pakuti ine ndakufotokozerani mlandu wanga.+
36 Choncho Yehova wanena kuti: “Ine ndikukuyankhira mlandu,+ ndipo ndidzakubwezerera chilango.+ Ndidzaphwetsa nyanja yake ndi zitsime zake.+