Salimo 71:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndikafuna kuimba nyimbo zokutamandani, pakamwa panga padzafuula mokondwera,+Ngakhalenso moyo wanga umene mwauwombola+ udzakutamandani. Yeremiya 50:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Wowawombola ndi wamphamvu,+ dzina lake ndi Yehova wa makamu.+ Iye sadzalephera kuwaweruzira mlandu wawo+ kuti apumitse dziko lawo+ ndiponso kusokoneza mtendere wa anthu okhala m’Babulo.”+
23 Ndikafuna kuimba nyimbo zokutamandani, pakamwa panga padzafuula mokondwera,+Ngakhalenso moyo wanga umene mwauwombola+ udzakutamandani.
34 Wowawombola ndi wamphamvu,+ dzina lake ndi Yehova wa makamu.+ Iye sadzalephera kuwaweruzira mlandu wawo+ kuti apumitse dziko lawo+ ndiponso kusokoneza mtendere wa anthu okhala m’Babulo.”+