Levitiko 26:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Koma ngakhale kuti padzachitika zonsezi, pamene iwo akukhala m’dziko la adani awo, sindidzawakana+ kapena kunyansidwa nawo+ moti n’kuwafafaniziratu, kuphwanya pangano langa+ ndi iwo, chifukwa ine ndine Yehova Mulungu wawo. Yeremiya 15:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Inu Yehova mukudziwa bwino mavuto anga.+ Ndikumbukireni+ ndipo mutembenuke ndi kundiyang’ana kuti mubwezere anthu ondizunza.+ Musandichotsere moyo wanga chifukwa chakuti simupsa mtima mwamsanga.+ Onani chitonzo chimene chili pa ine chifukwa cha dzina lanu.+ Maliro 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Taonani, inu Yehova. Inetu zandivuta. M’mimba mwanga mukubwadamuka.+Mtima wanga wasweka,+ pakuti ndapanduka kwambiri.+Panja, lupanga lapha+ ana. M’nyumba, anthu akufanso.+
44 Koma ngakhale kuti padzachitika zonsezi, pamene iwo akukhala m’dziko la adani awo, sindidzawakana+ kapena kunyansidwa nawo+ moti n’kuwafafaniziratu, kuphwanya pangano langa+ ndi iwo, chifukwa ine ndine Yehova Mulungu wawo.
15 Inu Yehova mukudziwa bwino mavuto anga.+ Ndikumbukireni+ ndipo mutembenuke ndi kundiyang’ana kuti mubwezere anthu ondizunza.+ Musandichotsere moyo wanga chifukwa chakuti simupsa mtima mwamsanga.+ Onani chitonzo chimene chili pa ine chifukwa cha dzina lanu.+
20 Taonani, inu Yehova. Inetu zandivuta. M’mimba mwanga mukubwadamuka.+Mtima wanga wasweka,+ pakuti ndapanduka kwambiri.+Panja, lupanga lapha+ ana. M’nyumba, anthu akufanso.+