Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 4:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Pamapeto pake, mawu amenewa akadzakwaniritsidwa pa inu, n’kukhala pamavuto aakulu, mudzabwereradi kwa Yehova Mulungu wanu+ ndi kumvetsera mawu ake.+

  • Salimo 80:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Inu Mulungu, tibwezeretseni mwakale.+

      Walitsani nkhope yanu kuti tipulumutsidwe.+

  • Salimo 85:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Tisonkhanitseni ndi kutibwezeretsa mwakale, inu Mulungu wa chipulumutso chathu,+

      Ndipo tichotsereni mkwiyo wanu.+

  • Yeremiya 31:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 “Ndamva Efuraimu akudzilirira+ kuti, ‘Mwandidzudzula kuti ndiwongolere.+ Ndinali ngati mwana wa ng’ombe wosaphunzitsidwa.+ Ndithandizeni kubwerera ndipo ndidzabwereradi,+ pakuti inu ndinu Yehova Mulungu wanga.+

  • Yeremiya 32:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 ‘Inetu ndikuwasonkhanitsa pamodzi kuchokera kumayiko onse kumene ndinawabalalitsira nditakwiya, kupsa mtima ndiponso ndili ndi ukali waukulu.+ Ndidzawabwezeretsa m’dziko lino ndi kuwachititsa kukhala mwamtendere.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena