Salimo 137:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iwe mwana wamkazi wa Babulo, amene udzafunkhidwa,+Wodala ndi amene adzakubwezera+Zimene iwe watichitira.+ Yesaya 51:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndidzachiika m’manja mwa amene akukuvutitsa,+ amene akukuuza kuti, ‘Werama kuti tiwolokere pamsana pako,’ amene akuona msana wako ngati pansi popondapo, ndiponso ngati njira yowolokerapo.”+
8 Iwe mwana wamkazi wa Babulo, amene udzafunkhidwa,+Wodala ndi amene adzakubwezera+Zimene iwe watichitira.+
23 Ndidzachiika m’manja mwa amene akukuvutitsa,+ amene akukuuza kuti, ‘Werama kuti tiwolokere pamsana pako,’ amene akuona msana wako ngati pansi popondapo, ndiponso ngati njira yowolokerapo.”+