Salimo 81:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho ndinawasiya kuti apitirize kuumitsa mtima wawo.+Iwo anapitiriza kuyenda mu nzeru zawo.+ Yesaya 66:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ineyo ndidzasankha njira zowazunzira.+ Ndidzawabweretsera zinthu zimene amachita nazo mantha+ chifukwa ndinaitana koma palibe amene anayankha. Ndinalankhula koma palibe amene anamvera.+ Iwo anapitiriza kuchita zinthu zoipa pamaso panga ndipo anasankha zinthu zimene sindisangalala nazo.”+ Aroma 1:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Chotero malinga ndi zilakolako za m’mitima mwawo, Mulungu anawasiya kuti achite zonyansa,+ kuti matupi awo+ achitidwe chipongwe.+ 2 Atesalonika 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ichi n’chifukwa chake Mulungu walola kuti iwo anyengedwe ndipo azikhulupirira bodza,+
4 Ineyo ndidzasankha njira zowazunzira.+ Ndidzawabweretsera zinthu zimene amachita nazo mantha+ chifukwa ndinaitana koma palibe amene anayankha. Ndinalankhula koma palibe amene anamvera.+ Iwo anapitiriza kuchita zinthu zoipa pamaso panga ndipo anasankha zinthu zimene sindisangalala nazo.”+
24 Chotero malinga ndi zilakolako za m’mitima mwawo, Mulungu anawasiya kuti achite zonyansa,+ kuti matupi awo+ achitidwe chipongwe.+