Salimo 119:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndasunga mosamala mawu anu mumtima mwanga,+Kuti ndisakuchimwireni.+ Luka 8:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Komano zogwera panthaka yabwino, ndi anthu amene pambuyo pomva mawuwo ndi mtima woona+ komanso wabwino, amawagwiritsitsa ndi kubereka zipatso mwa kupirira.+
15 Komano zogwera panthaka yabwino, ndi anthu amene pambuyo pomva mawuwo ndi mtima woona+ komanso wabwino, amawagwiritsitsa ndi kubereka zipatso mwa kupirira.+