Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 2:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Ndiyeno zinali kuchitika kuti woweruza akamwalira, ana a Isiraeli anali kupatuka ndi kuchita zinthu zowawonongetsa kuposanso makolo awo. Anali kuchita zimenezi mwa kutsatira milungu ina, kuitumikira ndi kuigwadira.+ Iwo sanasiye zochita zawozo ndiponso khalidwe lawo la unkhutukumve.+

  • 2 Mbiri 21:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 koma wayenda m’njira ya mafumu a Isiraeli+ n’kuchititsa Yuda ndi anthu okhala mu Yerusalemu kuchita zoipa,+ monga mmene a m’nyumba ya Ahabu anachititsira ena kuchita zoipa,+ ndiponso wapha ngakhale abale ako a m’nyumba ya bambo ako amene anali abwino kuposa iwe,+

  • Yeremiya 7:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Ukawauze kuti, ‘Uwu ndiwo mtundu umene anthu ake sanamvere mawu a Yehova Mulungu wawo,+ ndipo sanamvere chilango.*+ Palibe munthu wokhulupirika pakati pawo, ndipo satchulanso n’komwe za kukhulupirika.’+

  • Yeremiya 13:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Chigololo chako,+ kumemesa* kwako,+ khalidwe lako lotayirira la uhule, zonsezi zidzaonekera. Ndaona zinthu zako zonyansa pamapiri kuthengo.+ Tsoka kwa iwe Yerusalemu! Sungakhale woyera.+ Kodi udzakhalabe wosayera kufikira liti?”+

  • Machitidwe 7:51
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 51 “Anthu okanika inu ndi osachita mdulidwe wa mumtima+ ndi m’makutu. Nthawi zonse mumatsutsana ndi mzimu woyera. Mmene anachitira makolo anu inunso mukuchita chimodzimodzi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena