Miyambo 19:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mumtima mwa munthu mumakhala zolinga zambiri,+ koma zolinga za Yehova n’zimene zidzakwaniritsidwe.+ Maliro 3:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Tsopano ndani ananenapo kuti chinthu chichitike, chinthucho n’kuchitikadi Yehova asanalamule?+
21 Mumtima mwa munthu mumakhala zolinga zambiri,+ koma zolinga za Yehova n’zimene zidzakwaniritsidwe.+