Levitiko 27:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ng’ombe kapena nkhosa iliyonse ya 10, pa nyama zonse zodutsa pansi pa ndodo,*+ iliyonse ya 10 iziperekedwa kwa Yehova ndipo izikhala yopatulika. Yeremiya 33:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Yehova wanena kuti, ‘Ziweto zidzadutsa pansi pa dzanja la munthu woziwerenga+ m’mizinda ya m’madera amapiri, m’mizinda ya m’chigwa,+ m’mizinda ya kum’mwera,+ m’dziko la Benjamini,+ m’madera ozungulira Yerusalemu+ ndi m’mizinda ya Yuda.’”+ Ezekieli 34:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “‘Koma inu nkhosa zanga, imvani zimene Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena. Iye wanena kuti: “Ine ndidzaweruza mwachilungamo pakati pa nkhosa ndi nkhosa inzake komanso pakati pa nkhosa zamphongo ndi mbuzi zamphongo.+
32 Ng’ombe kapena nkhosa iliyonse ya 10, pa nyama zonse zodutsa pansi pa ndodo,*+ iliyonse ya 10 iziperekedwa kwa Yehova ndipo izikhala yopatulika.
13 “Yehova wanena kuti, ‘Ziweto zidzadutsa pansi pa dzanja la munthu woziwerenga+ m’mizinda ya m’madera amapiri, m’mizinda ya m’chigwa,+ m’mizinda ya kum’mwera,+ m’dziko la Benjamini,+ m’madera ozungulira Yerusalemu+ ndi m’mizinda ya Yuda.’”+
17 “‘Koma inu nkhosa zanga, imvani zimene Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena. Iye wanena kuti: “Ine ndidzaweruza mwachilungamo pakati pa nkhosa ndi nkhosa inzake komanso pakati pa nkhosa zamphongo ndi mbuzi zamphongo.+