Salimo 89:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Sindidzaphwanya pangano langa,+Ndipo sindidzasintha mawu otuluka pakamwa panga.+