Yesaya 5:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yehova wa makamu adzakwezeka kudzera m’chiweruzo,+ ndipo Mulungu woona, Woyera,+ adzadziyeretsa kudzera m’chilungamo.+ Ezekieli 38:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndidzadzilemekeza, kudziyeretsa+ ndi kuchititsa kuti mitundu yambiri ya anthu indidziwe, ndipo iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.’+
16 Yehova wa makamu adzakwezeka kudzera m’chiweruzo,+ ndipo Mulungu woona, Woyera,+ adzadziyeretsa kudzera m’chilungamo.+
23 Ndidzadzilemekeza, kudziyeretsa+ ndi kuchititsa kuti mitundu yambiri ya anthu indidziwe, ndipo iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.’+