Mika 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma iwo sakudziwa maganizo a Yehova. Iwo sakumvetsa cholinga chake+ pakuti adzawasonkhanitsa ndithu ndi kuwaika pamalo opunthira ngati mmene munthu amasonkhanitsira tirigu amene angomumweta kumene.+ Mateyu 13:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Zilekeni zonse zikulire pamodzi mpaka nthawi yokolola. M’nyengo yokolola ndidzauza okololawo kuti, Choyamba sonkhanitsani namsongole ndi kumumanga m’mitolo kuti akatenthedwe.+ Mukatha mupite kukasonkhanitsa tirigu ndi kumuika m’nkhokwe yanga.’”+
12 Koma iwo sakudziwa maganizo a Yehova. Iwo sakumvetsa cholinga chake+ pakuti adzawasonkhanitsa ndithu ndi kuwaika pamalo opunthira ngati mmene munthu amasonkhanitsira tirigu amene angomumweta kumene.+
30 Zilekeni zonse zikulire pamodzi mpaka nthawi yokolola. M’nyengo yokolola ndidzauza okololawo kuti, Choyamba sonkhanitsani namsongole ndi kumumanga m’mitolo kuti akatenthedwe.+ Mukatha mupite kukasonkhanitsa tirigu ndi kumuika m’nkhokwe yanga.’”+