Salimo 68:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Monga mmene mphepo imauluzira utsi, inunso muwauluze chimodzimodzi.+Ngati mmene phula limasungunukira chifukwa cha moto,+Anthu oipa awonongeke ndi kuchotsedwa pamaso pa Mulungu.+ Salimo 112:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Woipa adzaona zimenezi ndipo adzasautsika.+ ש [Shin]Adzakukuta mano ndi kusungunuka.+ ת [Taw]Chikhumbo cha anthu oipa chidzatha.+
2 Monga mmene mphepo imauluzira utsi, inunso muwauluze chimodzimodzi.+Ngati mmene phula limasungunukira chifukwa cha moto,+Anthu oipa awonongeke ndi kuchotsedwa pamaso pa Mulungu.+
10 Woipa adzaona zimenezi ndipo adzasautsika.+ ש [Shin]Adzakukuta mano ndi kusungunuka.+ ת [Taw]Chikhumbo cha anthu oipa chidzatha.+