Salimo 106:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Iwo anakhala odetsedwa chifukwa cha ntchito zawo,+Zochita zawo zinawalowetsa m’makhalidwe oipa.+ Hoseya 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inetu ndimamudziwa bwino Efuraimu+ ndipo Isiraeli si wobisika kwa ine.+ Iwe Efuraimu ukuchita zachiwerewere ndi akazi+ ndipo Isiraeli wadziipitsa.+ Hoseya 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndaona zinthu zoopsa m’nyumba ya Isiraeli.+ Efuraimu akuchita dama mmenemo.+ Isiraeli wadziipitsa.+
3 Inetu ndimamudziwa bwino Efuraimu+ ndipo Isiraeli si wobisika kwa ine.+ Iwe Efuraimu ukuchita zachiwerewere ndi akazi+ ndipo Isiraeli wadziipitsa.+
10 Ndaona zinthu zoopsa m’nyumba ya Isiraeli.+ Efuraimu akuchita dama mmenemo.+ Isiraeli wadziipitsa.+