2 Mafumu 17:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Komabe, nawonso Ayudawo sanasunge malamulo a Yehova Mulungu+ wawo, koma anayenda motsatira malamulo amene Aisiraeli+ anapanga.
19 Komabe, nawonso Ayudawo sanasunge malamulo a Yehova Mulungu+ wawo, koma anayenda motsatira malamulo amene Aisiraeli+ anapanga.