Yeremiya 6:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Yehova wanena kuti: “Taonani! Anthu akubwera kuchokera kudziko la kumpoto. Pali mtundu wamphamvu umene udzadzutsidwa kuchokera kumalekezero a dziko lapansi.+ Yeremiya 12:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Cholowa changa+ chili ngati mbalame yanthenga zamitundumitundu, yodya nyama. Mbalame zodya nyama zaizungulira.+ Bwerani, sonkhanani pamodzi inu nyama zonse zam’tchire. Bwerani ndi anzanu kuti mudzaidye.+
22 Yehova wanena kuti: “Taonani! Anthu akubwera kuchokera kudziko la kumpoto. Pali mtundu wamphamvu umene udzadzutsidwa kuchokera kumalekezero a dziko lapansi.+
9 Cholowa changa+ chili ngati mbalame yanthenga zamitundumitundu, yodya nyama. Mbalame zodya nyama zaizungulira.+ Bwerani, sonkhanani pamodzi inu nyama zonse zam’tchire. Bwerani ndi anzanu kuti mudzaidye.+