Ekisodo 32:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho pa tsiku lotsatira, anthuwo anadzuka m’mamawa, ndi kuyamba kupereka nsembe zopsereza ndi zachiyanjano. Atatero, iwo anakhala pansi ndi kudya ndiponso kumwa. Kenako anaimirira n’kuyamba kusangalala.+ Hoseya 13:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iwe unakhuta chifukwa chakuti unali ndi zakudya zambiri.+ Unakhuta ndipo mtima wako unayamba kudzitukumula.+ N’chifukwa chake unandiiwala.+
6 Choncho pa tsiku lotsatira, anthuwo anadzuka m’mamawa, ndi kuyamba kupereka nsembe zopsereza ndi zachiyanjano. Atatero, iwo anakhala pansi ndi kudya ndiponso kumwa. Kenako anaimirira n’kuyamba kusangalala.+
6 Iwe unakhuta chifukwa chakuti unali ndi zakudya zambiri.+ Unakhuta ndipo mtima wako unayamba kudzitukumula.+ N’chifukwa chake unandiiwala.+