Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 20:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 “‘Munthu wochita chigololo ndi mkazi wa munthu wina, wachita chigololo ndi mkazi wa mnzake.+ Mwamuna ndi mkazi amene achita chigololowo aziphedwa ndithu.+

  • Deuteronomo 22:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 azim’bweretsa mtsikanayo pakhomo la nyumba ya bambo ake ndipo amuna a mumzindawo azim’ponya miyala kuti afe, chifukwa wachita chinthu chopusa ndi chochititsa manyazi mu Isiraeli,+ mwa kuchita uhule m’nyumba ya bambo ake.+ Motero muzichotsa woipayo pakati panu.+

  • Ezekieli 16:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 “‘Ndidzakupatsa chiweruzo chimene chimaperekedwa kwa akazi achigololo+ ndi kwa akazi okhetsa magazi,+ ndipo ndidzakupatsa magazi a mkwiyo ndi nsanje.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena