Oweruza 20:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho ndinatenga mdzakazi wanga ndi kum’duladula, n’kutumiza ziwalozo m’dera lililonse la cholowa cha Isiraeli.+ Ndinatero chifukwa iwo anachita khalidwe lotayirira+ komanso chinthu chopusa ndi chochititsa manyazi mu Isiraeli.+ Ezekieli 22:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mwa iwe muli anthu amiseche amene akukhetsa magazi.+ Iwo amadya chakudya choperekedwa nsembe kwa mafano m’mapiri.+ Achita khalidwe lotayirira mwa iwe.+
6 Choncho ndinatenga mdzakazi wanga ndi kum’duladula, n’kutumiza ziwalozo m’dera lililonse la cholowa cha Isiraeli.+ Ndinatero chifukwa iwo anachita khalidwe lotayirira+ komanso chinthu chopusa ndi chochititsa manyazi mu Isiraeli.+
9 Mwa iwe muli anthu amiseche amene akukhetsa magazi.+ Iwo amadya chakudya choperekedwa nsembe kwa mafano m’mapiri.+ Achita khalidwe lotayirira mwa iwe.+