Deuteronomo 13:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pamenepo Aisiraeli onse adzamva ndi kuchita mantha, ndipo sadzachita chinthu choipa chilichonse chofanana ndi chimenechi pakati panu.+ 2 Petulo 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anaweruzanso mizinda ya Sodomu ndi Gomora mwa kuinyeketsa ndi moto,+ kuti chikhale chitsanzo cha zinthu zimene zidzachitikire anthu osaopa Mulungu m’tsogolo.+
11 Pamenepo Aisiraeli onse adzamva ndi kuchita mantha, ndipo sadzachita chinthu choipa chilichonse chofanana ndi chimenechi pakati panu.+
6 Anaweruzanso mizinda ya Sodomu ndi Gomora mwa kuinyeketsa ndi moto,+ kuti chikhale chitsanzo cha zinthu zimene zidzachitikire anthu osaopa Mulungu m’tsogolo.+