Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 59:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Iye adzawapatsa mphoto mogwirizana ndi zochita zawo.+ Adani ake adzawapatsa mkwiyo ndipo anthu otsutsana naye adzawapatsa chilango chowayenerera.+ Zilumbanso adzazipatsa chilango choyenerera.+

  • Ezekieli 16:43
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 43 “‘Popeza sunakumbukire masiku a ubwana wako+ ndipo unandikwiyitsa ndi zinthu zonsezi,+ ineyo ndidzakubwezera malinga ndi zochita zako.+ Sudzachitanso khalidwe lako lotayirira komanso zinthu zako zonse zonyansa,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.

  • Aroma 2:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Iye adzaweruza aliyense malinga ndi ntchito zake motere:+

  • Agalatiya 6:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Musanyengedwe,+ Mulungu sapusitsika.+ Chilichonse chimene munthu wafesa, adzakololanso chomwecho.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena