Yeremiya 16:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ofedwa sadzapatsidwa chakudya chowatonthoza+ ndipo sadzapatsidwa zakumwa kuti awatonthoze pamaliro a bambo awo kapena mayi awo.+ Ezekieli 24:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Uuse moyo mosatulutsa mawu. Anthu akufa usawalire maliro.+ Uvale chovala chakumutu+ ndipo uvale nsapato zako.+ Usaphimbe ndevu zako zapamlomo,+ ndipo usadye chakudya chimene anthu angakupatse.”+
7 Ofedwa sadzapatsidwa chakudya chowatonthoza+ ndipo sadzapatsidwa zakumwa kuti awatonthoze pamaliro a bambo awo kapena mayi awo.+
17 Uuse moyo mosatulutsa mawu. Anthu akufa usawalire maliro.+ Uvale chovala chakumutu+ ndipo uvale nsapato zako.+ Usaphimbe ndevu zako zapamlomo,+ ndipo usadye chakudya chimene anthu angakupatse.”+