Yesaya 59:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tonsefe tikungolira ngati zimbalangondo ndipo tikungokhalira kubuula momvetsa chisoni ngati njiwa.+ Tinali kuyembekezera chilungamo+ koma sichinabwere. Tinali kuyembekezera chipulumutso koma chakhala nafe kutali.+
11 Tonsefe tikungolira ngati zimbalangondo ndipo tikungokhalira kubuula momvetsa chisoni ngati njiwa.+ Tinali kuyembekezera chilungamo+ koma sichinabwere. Tinali kuyembekezera chipulumutso koma chakhala nafe kutali.+