Deuteronomo 28:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ana ako aamuna ndi ana ako aakazi adzaperekedwa kwa anthu ena+ iwe ukuona ndipo udzawalakalaka nthawi zonse, koma manja ako adzakhala opanda mphamvu.+ Yeremiya 11:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Yehova wa makamu wanena kuti: “Tsopano ndikuwapatsa chilango. Anyamata adzafa ndi lupanga.+ Ana awo aamuna ndi aakazi adzafa ndi njala yaikulu.+
32 Ana ako aamuna ndi ana ako aakazi adzaperekedwa kwa anthu ena+ iwe ukuona ndipo udzawalakalaka nthawi zonse, koma manja ako adzakhala opanda mphamvu.+
22 Yehova wa makamu wanena kuti: “Tsopano ndikuwapatsa chilango. Anyamata adzafa ndi lupanga.+ Ana awo aamuna ndi aakazi adzafa ndi njala yaikulu.+