Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Nehemiya 4:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ndiyeno Nehemiya anati: “Inu Mulungu wathu, imvani+ mawu onyoza amene akutinenera.+ Bwezerani chitonzo chawocho+ pamutu pawo ndipo apititseni m’dziko laukapolo monga zofunkha.

  • Yobu 31:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Ngati ndinkasangalala ndi kutha kwa munthu amene ankadana nane kwambiri,+

      Kapena ngati ndinkakondwera chifukwa chakuti zoipa zam’gwera . . .

  • Miyambo 24:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Mdani wako akagwa usamasangalale ndipo akapunthwa, mtima wako usamakondwere,+

  • Obadiya 12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 “Iwe sunayenera kumangoonerera mosangalala pa tsiku limene m’bale wako anakumana ndi tsoka.+ Sunayenera kusangalala pa tsiku limene ana a Yuda anali kuwonongedwa.+ Sunayeneranso kulankhula modzitama pa tsiku limene iwo anamva zowawa.

  • Zefaniya 2:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 “Ndamva chitonzo cha Mowabu+ ndi mawu onyoza a ana a Amoni+ amene anali kunena kwa anthu anga. Iwo anali kuopseza anthu anga modzitukumula kuti awalanda dziko lawo.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena