Ezekieli 24:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pa tsiku limenelo udzatsegula pakamwa pako n’kulankhula ndi wothawayo+ ndipo sudzakhalanso chete.+ Choncho iwe udzakhala chizindikiro kwa iwo cholosera zam’tsogolo,+ ndipo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.”+ Ezekieli 33:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Tsopano madzulo, munthu wopulumuka uja asanafike, dzanja la Yehova linandikhudza.+ Ndipo Mulungu anatsegula pakamwa panga, wopulumuka uja asanafike m’mawa. Pakamwa panga panatseguka ndipo ndinayambanso kulankhula.+
27 Pa tsiku limenelo udzatsegula pakamwa pako n’kulankhula ndi wothawayo+ ndipo sudzakhalanso chete.+ Choncho iwe udzakhala chizindikiro kwa iwo cholosera zam’tsogolo,+ ndipo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.”+
22 Tsopano madzulo, munthu wopulumuka uja asanafike, dzanja la Yehova linandikhudza.+ Ndipo Mulungu anatsegula pakamwa panga, wopulumuka uja asanafike m’mawa. Pakamwa panga panatseguka ndipo ndinayambanso kulankhula.+