Mateyu 11:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Amene ali ndi makutu amve.+ Chivumbulutso 2:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Amene ali ndi makutu amve zimene mzimu+ ukunena ku mipingo.’+