Yesaya 30:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti amenewa ndi anthu opanduka,+ ana ochita zachinyengo,+ amene safuna kumva malamulo a Yehova,+ Yeremiya 5:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma anthu awa ali ndi mtima wouma ndi wopanduka. Achoka panjira yanga ndipo akuyenda m’njira yawo.+ Ezekieli 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Iwe mwana wa munthu, ukukhala pakati pa anthu opanduka+ omwe ali ndi maso koma saona,+ omwe ali ndi makutu koma samva,+ chifukwa ndi anthu opanduka.+
9 Pakuti amenewa ndi anthu opanduka,+ ana ochita zachinyengo,+ amene safuna kumva malamulo a Yehova,+
23 Koma anthu awa ali ndi mtima wouma ndi wopanduka. Achoka panjira yanga ndipo akuyenda m’njira yawo.+
2 “Iwe mwana wa munthu, ukukhala pakati pa anthu opanduka+ omwe ali ndi maso koma saona,+ omwe ali ndi makutu koma samva,+ chifukwa ndi anthu opanduka.+