Yesaya 23:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anthu adzamva chisoni chachikulu akadzamva za Turo,+ ngati mmene anamvera chisoni atamva za Iguputo.+ Ezekieli 27:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Pokulira adzaimba nyimbo yoimba polira+ yakuti,“‘“‘Ndani angafanane ndi Turo+ amene wawonongedwa pakati pa nyanja?+
5 Anthu adzamva chisoni chachikulu akadzamva za Turo,+ ngati mmene anamvera chisoni atamva za Iguputo.+
32 Pokulira adzaimba nyimbo yoimba polira+ yakuti,“‘“‘Ndani angafanane ndi Turo+ amene wawonongedwa pakati pa nyanja?+