Salimo 27:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ngati ndikanakhala wopanda chikhulupiriro poona ubwino wa Yehova m’dziko la anthu amoyo, ndikanataya chiyembekezo.+ Ezekieli 32:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Manda a Asuri ali pakatikati pa dzenje+ ndipo khamu lake lonse lazungulira manda akewo. Onsewo anaphedwa ndi lupanga chifukwa anachititsa mantha anthu m’dziko la anthu amoyo.
13 Ngati ndikanakhala wopanda chikhulupiriro poona ubwino wa Yehova m’dziko la anthu amoyo, ndikanataya chiyembekezo.+
23 Manda a Asuri ali pakatikati pa dzenje+ ndipo khamu lake lonse lazungulira manda akewo. Onsewo anaphedwa ndi lupanga chifukwa anachititsa mantha anthu m’dziko la anthu amoyo.